Philemon 1:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikukupempha chifukwa cha mwana wanga mwa Khristu, amene ndidachita ngati kumubala m'ndende muno. Iyeyu ndi Onesimo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndikudandaulira chifukwa cha mwana wanga, amene ndambala m'ndende, Onesimo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndikukupempha chifukwa cha mwana wanga Onesimo, amene ndamubala ndili mu unyolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndikudandaulira cifukwa ca mwana wanga, amene ndambala m'ndende, Onesimo,