Philemon 1:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati adakulakwirapo, kapena ali ndi ngongole kwa iwe, ngongoleyo ikhale yanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wokongola kanthu, kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati anakulakwira kapena kukongola kanthu kalikonse, ndidzalipira ineyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati anakulakwira kanthu, kapena wakongola kanthu, undiwerengere ine kameneko;