Philemon 1:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kalata yomweyinso tikulembera Afiya, mlongo wathu, ndi Arkipo, msilikali mnzathu pa nkhondo ya Mulungu, ndiponso mpingo wonse umene umasonkhana kunyumba kwanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kwa Afiya mlongoyo, ndi Arkipo msilikali mnzathu, ndi kwa Mpingo uli m'nyumba yako:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Apiya mlongo wathu, Arkipo msilikali mnzathu, ndiponso mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kwa Apiya mlongoyo, ndi Arkipo msilikari mnzathu, ndi kwa Mpingo uli m'nyumba yako;