Philippians 1:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Otsirizaŵa amamlalika chifukwa cha chikondi, popeza kuti amadziŵa kuti Mulungu adandikhazika muno kuti ndigwire ntchito yoteteza Uthenga Wabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ena atero ndi chikondi, podziwa kuti anandiika ndichite chokanira cha Uthenga Wabwino;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Olalikira ndi zolinga zabwinowa amachita izi mwachikondi, podziwa kuti ine ndili muno chifukwa cha kuteteza Uthenga Wabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ena atero ndi cikondi, podziwa kuti anandiika ndicite eokanira ca Uthenga Wabwino;