Philippians 1:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kwinakunso nkofunika kwambiri kuti ndikhale moyo chifukwa cha inuyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma kukhalabe m'thupi ndiko kufunika koposa, chifukwa cha inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso nʼkofunika kwambiri kuti ndikhalebe mʼthupi chifukwa cha inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma kukhalabe m'thupi ndiko kufunika koposa, cifukwa ca inu.