Philippians 1:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inunso mukumenya nkhondo yomwe ija imene mudandiwona ine ndikuimenya, yomwenso ndikumenyabe tsopano, monga mukumveramu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kukhala nacho inu chilimbano chomwechi mudachiona mwa ine, nimukumva tsopano chili mwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inunso mukudutsa mʼzowawa zomwe zija munaona ndikudutsamo inenso ndipo pano mukumva kuti ndikukumana nazobe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kukhala naco inu cilimbano comweci mudaciona mwa ine, nimukumva tsopano ciri mwa ine.