Philippians 3:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikuyesetsa kuchita zimenezi pokhulupirira kuti inenso ndidzakhala ndi moyo wosatha podzauka kwa akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati nkotheka ndikafikire kuuka kwa akufa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti nanenso ndidzaukitsidwe kwa akufa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngati nkotheka ndikafikire kuuka kwa akufa.