Philippians 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chenjera nawoni ochita zaugalu aja, ndiye kuti ochita zoipa, anthu omangodula thupi chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Penyererani agalu, penyererani ochita zoipa, penyererani choduladula;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chenjerani ndi agalu amenewa, anthu ochita zoyipa, anthu amene amadula thupi lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Penyererani agaru, penyererani ocita zoipa, penyererani coduladula;