Philippians 3:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo changu changa chinali chachikulu, kotero kuti ndinkazunza Mpingo. Kunena za chilungamo chopezeka pakutsata Malamulo, ineyo ndinali wopanda cholakwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga mwa changu, wolondalonda Mpingo; monga mwa chilungamo cha m'lamulo wokhala wosalakwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunena za changu changa, ndinkazunza mpingo. Kunena za chilungamo chopezeka chifukwa chotsata malamulo, ineyo ndinali wopanda cholakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga mwa cangu, wolondalonda Eklesia; monga mwa cilungamo ca m'lamulo wokhala wosalakwa ine.