Philippians 4:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndinali ku Tesalonika, mudatumiza kangapo zondithandiza pa zosoŵa zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti m'Tesalonikanso munanditumizira pa chosowa changa kamodzi kapena kawiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ngakhale pamene ndinali ku Tesalonika, munanditumizira kangapo zondithandiza pa zosowa zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti m'Tesalonikanso munanditumizira pa cosowa canga kamodzi kapena kawiri.