Philippians 4:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu Atate athu alemekezedwe mpaka muyaya. Amen.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kwa Mulungu ndi Atate wathu kukhale ulemerero kunthawi za nthawi, Amen.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Mulungu ndi Atate athu, kukhale ulemerero mpaka muyaya. Ameni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kwa Mulungu ndi Atate wathu kukhale ulemerero ku nthawi za nthawi, Amen.