Proverbs 1:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzati, “Tiye kuno, tikabisale kuti tiphe anthu, tiye tikalalire anthu osalakwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akanena, Idza nafe, tibisalire mwazi, tilalire osachimwa opanda chifukwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akadzati, “Tiye kuno; tikabisale kuti tiphe anthu, tikabisalire anthu osalakwa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akanena, Idza nafe, tibisalire mwazi, Tilalire osacimwa opanda cifukwa;