Proverbs 1:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tiyeni tiŵameze amoyo ngati manda, tiŵameze athunthu ngati anthu otsikira ku manda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
tiwameze ali ndi moyo ngati manda, ali amphumphu, ngati akutsikira kudzenje;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
tiwameze amoyo ngati manda, ndi athunthu ngati anthu otsikira mʼdzenje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tiwameze ali ndi moyo ngati manda, Ali amphumphu, ngati akutsikira kudzenje;