Proverbs 1:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero tidzapata zinthu zambiri zamtengowapatali, nyumba zathu tidzazidzaza ndi zofunkha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
tidzapeza chuma chonse cha mtengo wake, tidzadzaza nyumba zathu ndi zofunkha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero tidzapeza zinthu zosiyanasiyana zamtengowapatali ndi kudzaza nyumba zathu ndi zolanda;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tidzapeza cuma conse ca mtengo wace, Tidzadzaza nyumba zathu ndi zofunkha;