Proverbs 1:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja iwowo amangofuna zoipa zokhazokha, amathamangira kupha basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti mapazi ao athamangira zoipa, afulumira kukhetsa mwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwowatu amangofuna zoyipa zokhazokha, amathamangira kukhetsa magazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mapazi ao athamangira zoipa, Afulumira kukhetsa mwazi.