Proverbs 1:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu ameneŵa amangodzitchera okha msampha, m'menemo muli imfa yao yomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo awa abisalira mwazi waowao, alalira miyoyo yaoyao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu amenewa amangobisalira miyoyo yawo yomwe; amangodzitchera okha msampha!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo awa abisalira mwazi wao wao, alalira miyoyo yao yao.