Proverbs 1:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngothandiza kuti anthu adziŵe nzeru ndi mwambo, kuti amvetse mau a matanthauzo ozama,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudziwa nzeru ndi mwambo; kuzindikira mau ozindikiritsa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi yothandiza kuti munthu adziwe nzeru ndi malangizo; kuti amvetse mawu a matanthauzo ozama;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kudziwa nzeru ndi mwambo; Kuzindikira mau ozindikiritsa;