Proverbs 1:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uphungu wanga simudaulabadire, kudzudzula kwanga simudakusamale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma munapeputsa uphungu wanga wonse, ndi kukana kudzudzula kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uphungu wanga munawunyoza. Kudzudzula kwanga simunakusamale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munapeputsa uphungu wangawonse, Ndi kukana kudzudzula kwanga.