Proverbs 1:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamene mantha adzakukunthani ngati namondwe, pamene tsoka lidzakufikirani ngati kamvulumvulu, pamene mavuto ndi masautso adzakugwerani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakudza mantha anu ngati mphepo yopasula, ndi pofika tsoka lanu ngati kamvulumvulu; pakudza kwa inu vuto ndi nsautso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwonongeko chikadzakugwerani ngati namondwe, tsoka likadzakufikirani ngati kamvuluvulu, mavuto ndi masautso akadzakugwerani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakudza mantha anu ngati mphepo yopasula, Ndi pofika tsoka lanu ngati kabvumvulu; Pakudza kwa inu bvuto ndi nsautso.