Proverbs 1:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti alandire mwambo wochita zinthu mwanzeru, akhale angwiro, achilungamo ndi osakondera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kulandira mwambo wakusamalira machitidwe, chilungamo, chiweruzo ndi zolunjika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti alandire malangizo othandiza kuti achite zinthu mwanzeru, akhale wangwiro, wachilungamo ndiponso wosakondera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kulandira mwambo wakusamalira macitidwe, Cilungamo, ciweruzo ndi zolunjika;