Proverbs 1:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
popeza kuti simudasamale malangizo anga, ndipo mudanyoza kudzudzula kwanga konse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anakana uphungu wanga, nanyoza kudzudzula kwanga konse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
popeza iwo sanasamale malangizo anga ndipo ananyoza chidzudzulo changa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakana uphungu wanga, Nanyoza kudzudzula kwanga konse;