Proverbs 1:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu opusa amaphedwa chifukwa cha kusokera kwao. Zitsiru zimadziwononga zokha nkudzitama kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti kubwerera m'mbuyo kwa achibwana kudzawapha; ndipo mphwai za opusa zidzawaononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti anthu osachangamuka amaphedwa chifukwa cha kusochera kwawo, ndipo zitsiru zimadziwononga zokha chifukwa cha mphwayi zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti kubwerera m'mbuyo kwa acibwana kudzawapha; Ndipo mphwai za opusa zidzawaononga.