Proverbs 1:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngophunzitsa anthu wamba nzeru za kuchenjera, ndi achinyamata kudziŵa zinthu ndi kulingalira bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuchenjeza achibwana, kuphunzitsa mnyamata kudziwa ndi kulingalira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi yothandiza munthu wamba kuti aphunzire nzeru za kuchenjera, achinyamata kudziwa zinthu bwino ndi kulingalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kucenjeza acibwana, Kuphunzitsa mnyamata kudziwa ndi kulingalira;