Proverbs 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi oti wanzeru akaŵamva, aonjezere kuphunzira kwake, ndipo munthu womvetsa zinthu apate luso,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti wanzeru amve, naonjezere kuphunzira; ndi kuti wozindikira afikire kuuphungu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wanzeru amvetse bwino miyamboyi kuti awonjezere kuphunzira kwake, ndi munthu womvetsa zinthu bwino apatepo luso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti wanzeru amve, naonjezere kuphunzira; Ndi kuti wozindikira afikire kuuphungu;