Proverbs 1:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti azimvetsa miyambi ndi mafanizo, mau a anthu anzeru ndi mikuluŵiko yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuzindikira mwambi ndi tanthauzo lake, mau a anzeru, ndi zophiphiritsa zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti azimvetsa miyambi ndi mafanizo, mawu a anthu anzeru ndi mikuluwiko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuzindikira mwambi ndi tanthauzo lace, Mau a anzeru, ndi zophiphiritsa zao.