Proverbs 1:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, umvere zimene bambo wako akukulangiza, usakane zimene mai wako akukuphunzitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, tamva mwambo wa atate wako, ndi kusasiya chilangizo cha amai ako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, mvera malangizo a abambo ako ndipo usakane mawu okuwongolera a amayi ako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, tamva mwambo wa atate wako, Ndi kusasiya cilangizo ca amako