Proverbs 13:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chipongwe cha osasamala za anzao chimadzetsa mkangano, koma omvera malangizo a anzao ndiwo ali ndi nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudzikuza kupikisanitsa; koma omwe anauzidwa uphungu ali ndi nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chipongwe chosamalabadirako za anthu ena chimadzetsa mikangano, koma womva malangizo a anzawo ndiwo ali ndi nzeru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kudzikuza kupikisanitsa; Koma omwe anauzidwa uphungu ali ndi nzeru.