Proverbs 13:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maphunzitso a anthu anzeru ali ngati kasupe wa moyo, amathandiza anthu kuti asakodwe mu msampha wa imfa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Malamulo a wanzeru ndiwo kasupe wa moyo, apatutsa kumisampha ya imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malangizo a munthu wanzeru ali ngati kasupe wamoyo; amathandiza munthu kuti asakondwe mu msampha wa imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Malamulo a wanzeru ndiwo kasupe wa moyo, Apatutsa ku misampha ya imfa.