Proverbs 13:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chinthu chochilakalaka chikachitikadi, chimasangalatsa mtima. Koma kuleka zoipa kuli ngati chinthu chonyansa kwa zitsiru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifuniro chikondweretsa moyo chitachitidwa; koma kusiya zoipa kunyansa opusa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chinthu chochilakalaka chikachitika chimasangalatsa mtima, koma zitsiru zimadana ndi kuleka zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifuniro cikondweretsa moyo citacitidwa; Koma kusiya zoipa kunyansa opusa,