Proverbs 13:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wabwino amapeza nako phindu kulankhula kwake, koma anthu onyenga amalakalaka zandeu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu adzadya zabwino ndi zipatso za m'kamwa mwake; koma moyo wa achiwembu udzadya chiwawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu amapeza zinthu zabwino chifukwa cha mawu ake, koma anthu osakhulupirika amalakalaka zachiwawa basi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu adzadya zabwino ndi zipatso za m'kamwa mwace; Koma moyo wa aciwembu udzadya ciwawa.