Proverbs 13:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wabwino amasiyira zidzukulu zake choloŵa, koma chuma cha munthu woipa amachilandira ndi anthu abwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wabwino asiyira zidzukulu zake cholowa chabwino; koma wochimwa angosungira wolungama chuma chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wabwino amasiyira zidzukulu zake cholowa, koma chuma cha munthu wochimwa amachilandira ndi olungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wabwino asiyira zidzukulu zace colowa cabwino; Koma wocimwa angosungira wolungama cuma cace.