Proverbs 13:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'tsala la munthu wosauka mumalola chakudya chambiri, koma anthu opanda chilungamo amalanda chakudyacho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kulima kwa osauka muli zakudya zambiri; koma zinazo zimaonongeka posowa chiweruzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsala la munthu wosauka limalola chakudya chambiri, koma anthu opanda chilungamo amachilanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kulima kwa osauka muli zakudya zambiri; Koma zinazo zimaonongeka posowa ciweruzo.