Proverbs 13:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wabwino ali nazo zokwanira zoti adye nkukhuta, koma m'mimba mwa munthu woipa mumakhala pululu ndi njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolungama adya nakhutitsa moyo wake; koma mimba ya oipa idzasowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wolungama amakhala ndi zakudya zoti adye nʼkukhuta, koma mʼmimba mwa munthu woyipa mumakhala pululu ndi njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolungama adya nakhutitsa moyo wace; Koma mimba ya oipa idzasowa.