Proverbs 13:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amagwira pakamwa pake amasunga moyo wake, koma amene amangolakatika amaonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wogwira pakamwa pake asunga moyo wake; koma woyasamula milomo yake adzaonongeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amene amagwira pakamwa pake amateteza moyo wake, koma amene amayankhula zopanda pake adzawonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wogwira pakamwa pace asunga moyo wace; Koma woyasamula milomo yace adzaonongeka.