Proverbs 13:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu waulesi amakhumbira zinthu koma sapeza kanthu, m'menemo munthu wakhama amalemera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wa waulesi ukhumba osalandira kanthu; koma moyo wa akhama udzalemera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu waulesi amakhumbira zinthu koma sapeza kanthu, koma munthu wakhama adzalemera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wa wolesi ukhumba osalandira kanthu; Koma moyo wa akhama udzalemera.