Proverbs 13:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wokonda Mulungu amadana ndi bodza, koma zochita za munthu woipa zimanyansa ndipo zimachititsa manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolungama ada mau onama; koma woipa anyansa, nadzichititsa manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wolungama amadana ndi zabodza, koma zochita za munthu woyipa zimanyansa ndiponso zimachititsa manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolungama ada mau onama; Koma woipa anyansa, nadzicititsa manyazi,