Proverbs 13:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wina amadziyesa wolemera, m'menemo alibe nkanthu komwe. Wina amadziyesa wosauka, m'menemo ali nchuma chochuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alipo wodziyesa wolemera, koma alibe kanthu; alipo wodziyesa wosauka, koma ali ndi chuma chambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wina amadziyesa kuti ndi wolemera chonsecho alibe kanthu kalikonse; munthu wina amaoneka ngati wosauka chonsecho ali ndi chuma chambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alipo wodziyesa wolemera, koma alibe kanthu; Alipo wodziyesa wosauka, koma ali ndi cuma cambiri.