Proverbs 15:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amasiya njira yabwino adzalangidwa koopsa. Amene amadana ndi kudzudzula adzafa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wosiya njira adzalangidwa mowawa; wakuda chidzudzulo adzafa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene amasiya njira yabwino adzalangidwa koopsa. Odana ndi chidzudzulo adzafa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wosiya njira adzalangidwa mowawa; Wakuda cidzudzulo adzafa.