Proverbs 15:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Manda ndi chiwonongeko ndi zosabisika kwa Mulungu, nanji tsono mitima ya anthu!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumanda ndi kuchionongeko kuli pamaso pa Yehova; koposa kotani nanga mitima ya ana a anthu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Manda ndi chiwonongeko ndi zosabisika pamaso pa Yehova, nanji mitima ya anthu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumanda ndi kucionongeko kuli pamaso pa Yehova; Koposa kotani nanga mitima ya ana a anthu?