Proverbs 15:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wa munthu womvetsa zinthu umafunitsitsa ndithu kudziŵa zambiri, koma m'kamwa mwa anthu opusa zauchitsiru zili pha!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wa wozindikira ufunitsa kudziwa; koma m'kamwa mwa opusa mudya utsiru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wa munthu wozindikira zinthu umafunafuna nzeru, koma pakamwa pa zitsiru pamadya uchitsiru wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wa wozindikira ufunitsa kudziwa; Koma m'kamwa mwa opusa mudya utsiru.