Proverbs 15:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuli bwino kudyera masamba pali chikondi, kupambana kudyera nyama ya ng'ombe yonenepa pali chidani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudya masamba, pali chikondano, kuposa ng'ombe yonenepa pali udani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuli bwino kudyera ndiwo zamasamba pamene pali chikondi, kusiyana ndi kudyera nyama yangʼombe yonenepa pamene pali udani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kudya masamba, pali cikondano, Kuposa ng'ombe yonenepa pali udani.