Proverbs 15:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Njira ya munthu waulesi ndi yoŵirira ndi minga, koma njira ya munthu wolungama imakhala ngati mseu wosalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mayendedwe a waulesi akunga linga laminga, koma njira ya oongoka mtima iundidwa ngati mseu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Njira ya munthu waulesi ndi yowirira ndi mtengo waminga, koma njira ya munthu wolungama ili ngati msewu waukulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mayendedwe a wolesi akunga Hnga laminga, Koma njira ya oongoka mtima iundidwa ngati mseu.