Proverbs 15:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau a anthu anzeru amapatsa nzeru, koma pakamwa pa opusa pamatulutsa zauchitsiru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lilime la anzeru linena bwino zomwe adziwa; koma m'kamwa mwa opusa mutsanulira utsiru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wanzeru amayankhula zinthu za nzeru, koma pakamwa pa zitsiru pamatulutsa za uchitsiru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lilime la anzeru linena bwino zomwe adziwa; Koma m'kamwa mwa opusa mutsanulira utsiru.