Proverbs 15:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanzeru amakondweretsa atate ake, koma mwana wopusa amanyoza amai ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwana wanzeru akondweretsa atate wake; koma munthu wopusa apeputsa amake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanzeru amakondweretsa abambo ake, koma mwana wopusa amanyoza amayi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwana wanzeru akondweretsa atate wace; Koma munthu wopusa apeputsa amace.