Proverbs 15:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uchitsiru umakondweretsa munthu wopanda nzeru, koma munthu womvetsa zinthu amatsata zolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wosowa nzeru akondwera ndi utsiru; koma munthu wozindikira aongola mayendedwe ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uchitsiru umakondweretsa munthu wopanda nzeru, koma munthu womvetsa zinthu amayenda mowongoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wosowa nzeru akondwera ndi utsiru; Koma munthu wozindikira aongola mayendedwe ace.