Proverbs 15:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuyankha mokhoza kumakondwetsa munthu, ndipo mau onena pa nthaŵi yake amakoma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akondwera ndi mayankhidwe a m'kamwa mwake; ndi mau a pa nthawi yake kodi sali abwino?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu amakondwera ndi kuyankha koyenera, ndipo mawu onena pa nthawi yake ndi okoma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akondwera ndi mayankhidwe a m'kamwa mwace; Ndi mau a pa nthawi yace kodi sali abwino?