Proverbs 15:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Njira yopita ku moyo imakamufikitsa ku ntchito zangwiro, kuti alewe malo a anthu akufa kunsiko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anzeru ayesa njira yamoyo yokwerakwera, kuti apatuke kusiya kunsi kwa manda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wanzeru amatsata njira yopita ku moyo kuti apewe malo okhala anthu akufa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anzeru ayesa njira yamoyo yokwerakwera, Kuti apambuke kusiya kunsi kwa manda.