Proverbs 15:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amapasula nyumba ya munthu wonyada, koma amasamalira kadziko ka mkazi wamasiye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adzapasula nyumba ya wonyada; koma adzalembera mkazi wamasiye malire ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amapasula nyumba ya munthu wonyada koma amasamalira malo a mkazi wamasiye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adzapasula nyumba ya wonyada; Koma adzalembera mkazi wamasiye malire ace,