Proverbs 15:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maganizo a anthu oipa amamnyansa Chauta, koma mau a anthu olungama amamkondweretsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ziwembu zoipa zinyansa Yehova; koma oyera mtima alankhula mau okondweretsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maganizo a anthu oyipa amamunyansa Yehova, koma mawu a anthu oyera mtima amamusangalatsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ziwembu zoipa zinyansa Yehova; Koma oyera mtima alankhula mau okondweretsa.