Proverbs 15:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wofunafuna phindu monyenga amavutitsa banja lake, koma munthu wodana ndi ziphuphu adzapeza bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wopindula monyenga avuta nyumba yake; koma wakuda mitulo adzakhala ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wofuna phindu mwachinyengo amavutitsa banja lake, koma wodana ndi ziphuphu adzakhala ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wopindula monyenga abvuta nyumba yace; Koma wakuda mitulo adzakhala ndi moyo.